Kupyolera m’dongosolo la banja la padziko lapansi, Mulungu watidziŵitsa zenizeni zake—banja lakumwamba.
Mulungu adalenga zolengedwa zambiri kuti zilandire moyo kudzera mwa amayi awo. Izi zinali kutionetsa kuti moyo wosatha umachokera kwa Mulungu Amayi.
Chifukwa chimene Yesu anatsindika za chikondi ndi kubwera padziko lino lapansi kudzafunafuna otayika ndi chifukwa chakuti ndife a m’banja lakumwamba. Ichi ndi chifukwa chake, mu moyo wathu wachikhulupiriro, timatchulana abale ndi alongo.
Kuchokera ku Genesis mpaka Chivumbulutso, Mulungu Elohim anachitira umboni kambirimbiri. Pokhapo mwa Mulungu Elohim—Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi, m’mene banja lakumwamba lingakhoze kukhala lathunthu.
amene atumikira chifaniziro ndi mthunzi wa zakumwambazo monga Mose achenjezedwa m’mene anafuna kupanga chihema: pakuti, Chenjera, ati, uchite zonse monga mwa chitsanzocho chaonetsedwa kwa iwe m’phiri.
Ahebri 8:5
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi