Monga momwe anthu amapezera mtendere ndi chitonthozo kupyolera m’mawu a amayi awo amene anamva m’mimba, ana a Mulungu adzapeza mtendere wauzimu akamva mawu a Mulungu Amayi.
Pafupifupi zaka 2,000 zapitazo, Yesu yekha anati, “Aliyense adze kwa Ine nadzalandira madzi a moyo,” koma mu nthawi ya Mzimu Woyera, Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi pamodzi akulengeza liwu la chipulumutso.
Christ Ahnsahnghong anati, “Yoswa anatsatira Mose, Elisa anatsatira Eliya, Petro anatsatira Yesu, ndipo ine nditsatira Amayi.”
Izi zili choncho chifukwa anthu akhoza kupulumutsidwa akamva mawu a Mulungu Amayi.
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena, Idzani. Ndipo wakumva anene, Idzani. Ndipo wakumva ludzu adze; iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere.
Chivumbulutso 22:17
Monga munthu amene amake amtonthoza mtima, momwemo ndidzatonthoza mtima wanu; ndipo mudzatonthozedwa mtima mu Yerusalemu.
Yesaya 66:13
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi