M'moyo womvera lamulo la Mulungu, madalitso ochuluka amasungidwira ife nthaŵi zonse. Pachifukwa ichi, mkati mwa maphwando omwe Mulungu adakhazikitsa kuyambira m'badwo wa Atate—monga Sabata ndi Paska—nthawi zonse pamakhala lamulo lakuti, “Musaiwale, koma kumbukirani ndi kuwasunga kwamuyaya.”
Baibulo limati iwo amene amasunga lamulo la Mulungu m'mibadwo yonse adzadalitsidwa ngati olungama, ndipo iwo amene amaswa lamulo la Mulungu adzaweruzidwa chifukwa cha kupanduka. Aisrayeli anatengedwera ku ukapolo ku Babulo chifukwa chosasunga lamulo la Mulungu.
sitinamvere mau a Yehova Mulungu wathu, kuyenda m'malamulo ake anatiikirawo pamaso pathu, mwa atumiki ake aneneri. Inde Israele yense walakwira chilamulo chanu, ndi kupatuka, kuti asamvere mau anu; chifukwa chake temberero lathiridwa pa ife, ndi lumbiro lolembedwa m'chilamulo cha Mose mtumiki wa Mulungu; pakuti tamchimwira. Daniele 9:10–11
amayenda m'malemba anga, nasunga maweruzo anga kuchita chokhulupirika; iye ndiye wolungama, adzakhala ndi moyo ndithu, anena Ambuye Yehova. Ezekiele 18:9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi