Mulungu adasankha kale mayina ndi matsiku a maphwando onse a Chipangano Chakale kudzera mchilamulo cha Mose zaka 3,500 zapitazo ndipo adatilamulira kuti tisunge Tsiku la Pentekoste pa tsiku la 50 kuchokera pa Tsiku la kuuka kwa akufa (Phwando la zipatso zoyambirira).
Pambuyo pa kuuka kwa Yesu,ophunzira adapemphera kolimba matsiku
Khumi kuyambira tsiku lakukwera kumwamba ndikulandila mzimu woyera
pa tsiku la Pentekoste; iwo adawona ntchito yayikulu ya mzimu woyera pomwe
anthu zikwi zitatu adatsogozedwa ku chipulumutso tsiku limodzi.
Momwemonso, oyera a Mpingo wa Mulungu akusunga Tsiku la Pentekoste malinga ndi mawu ndikuchitira umboni ku dziko lonse lapansi za apulumutsi mu M'badwo wa Mzimu Woyera,
Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, kudzera mu Mzimu Woyera wa mvula yamasika, kudzutsa anthu ndi mtima wawo wonse ndi malingaliro.
Komatu mudzalandira mphamvu, Mzimu Woyera atadza pa inu: ndipo mudzakhala mboni zanga m'Yerusalemu, ndi m'Yudeya lonse, ndi m'Samariya, ndi kufikira malekezero ake a dziko. Machitidwe 1:8
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi