Pa Tsiku la chitetezero, anthu akhoza kulandira
chisomo cha chikhululukiro kuchokera kwa Mulungu
chifukwa cha machimo onse amene anachita kumwamba
ndi mosadziwa padziko lapansi pano, mwa kulapa
masiku khumi kuyambira pa Phwando la Malipenga.
Ndi tsiku lodalitsika
pamene njira yobwerera ku ufumu
wakumwamba yatsegulidwa.
Monga anamwali anzeru omwe adakonza nyali zawo
ndi mafuta pa phwando laukwati, mamembala a Mpingo
wa Mulungu amakonza nyali zawo ndi chitsimikizo mu
chowonadi cha pangano latsopano, ndi mafuta ndi
chikhulupiriro cholimba mwa Khristu Ahnsahnghong ndi
Mulungu Amayi, ndipo molimba mtima amachitira
umboni choonadi chotsimikizika ku dziko lonse lapansi.
usaope, pakuti Ine ndili pamodzi ndi iwe;
usaopsedwe, pakuti Ine ndine Mulungu wako;
ndidzakulimbitsa; inde, ndidzakuthangata;
inde, ndidzakuchirikiza ndi dzanja
langa lamanja la chilungamo.
Yesaya 41:10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi