Nthawi ya Mose, anthu analumidwa ndi njoka zamoto ndipo adafa. M'malo mokhulupirira mawu a Mulungu, “Yense wakuyipenya njoka ya mkuwa adzakhala ndi moyo,” anapembedza njokayo zaka mazana, poganiza kuti inali ndi mphamvu yozizwitsa. Pambuyo pake, Mfumu Hezekiya ataiphwanya, Mulungu anamutamanda.
Si mtanda umene unatipulumutsa, koma Yesu.
Mpingo womwe umakhazikitsa mtanda udzawonongedwa. Ndiye, Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse Mpingo wa Mulungu siukhazikitsa mtanda koma umasunga Paska wa pangano latsopano.
Ndipo monga Mose anakweza njoka m'chipululu, chotero Mwana wa Munthu ayenera kukwezedwa; kuti yense wakukhulupirira akhale nao moyo wosatha mwa Iye. Yohane 3:14–15
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi