Monga momwe Yesu adapilira ndikugonjetsa kunyozedwa, kukanidwa ndi anthu, ndi kuperekedwa ndi ophunzira Ake, ndikuzunzika pamtanda zonsezi chifukwa cha ana Ake okondedwa, ifenso, tiyenera kunyamula mtanda wathu ndikutsata njira ya Yesu.
Kudzera mu chikondwerero cha Mkate Wopanda Chotupitsa, tiyenera kukumbukira masautso a Yesu Khristu ndikuganiza chisautso cha Khristu Ahnsahnghong yemwe adabweranso kachiwiri. Tikamatsata Khristu panjira Yake, kuthokoza munthawi zonse, Mulungu amasintha zopinga ngati Nyanja Yofiira kukhala chida chachisomo.
Pamenepo Yesu anati kwa ophunzira ake, “Ngati wina aliyense abwera pambuyo panga ayenera kudzikana ndi kutenga mtanda wake ndi kunditsata Ine.Pakuti aliyense amene afuna kupulumutsa moyo wake adzawutaya koma aliyense amene ataya moyo wake chifukwa cha Ine adzawupeza.” Mateyu 16:24–25
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi