Phwando la Mkate Wopanda Chotupitsa m’Chipangano
Chakale ndi kukumbukira zovuta zomwe Aisrayeli
anakumana nazo zaka 3,500 zapitazo; atatha kuchita
Paska, anatuluka mu Ejipito m’mawa mwake
ndipo anadutsa m’mavuto mpaka anawoloka Nyanja Yofiira.
Izi zinatumikira monga mthunzi wa zowawa,
ndi nsembe zimene Yesu Khristu akanakomana
nazo; atamaliza Paska, adamva zowawa
ndipo adapachikidwa tsiku lotsatira.
Kukanidwa ndi kuperekedwa ndi ophunzira omwe adanena
kuti, "Ife tidzakutsatani mpaka imfa," kunyozedwa ndi
kusekedwa ndi adani ambiri, ndipo potsirizira pake kupachikidwa
pa mtanda - uyu ndi Khristu Ahnsahnghong wozunzika,
Mpulumutsi mu m’badwo wa Mzimu Woyera, unadutsa zaka 2,000 zapitazo.
Tsopano ndi nthawi yomwe timasowa
chikhulupiriro chomwe chimazindikira
chikondi chake ndikunyamula mtanda wathu.
Pomwepo Yesu anati kwa ophunzira ake,
Ngati munthu afuna kudza pambuyo
panga, adzikane yekha, natenge
mtanda wake, nanditsate Ine.
Pakuti iye amene afuna kupulumutsa
moyo wake adzautaya: koma iye amene
ataya moyo wake chifukwa cha Ine, adzaupeza.
Mateyu 16:24-25
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi