Popanda kudziwa tanthauzo la moyo, anthu amangoyendayenda, omangidwa ndi ntchito zawo ndipo amakumana ndi imfa. Komabe, pali chinthu chofunika chobisika m'moyo wathu.
Baibulo limaphunzitsa kuti imfa imatanthauza “kubwerera” kumwamba ndipo anthu anali kumwamba Mulungu asanalenge dziko lapansi. Tikasunga Paska, amene Mzimu ndi Mkwatibwi—Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai—anatipatsa, tikhoza kubwerera kumudzi kwathu, kumwamba.
Iwo onse adamwalira m'chikhulupiriro, osalandira malonjezano, komatu adawaona ndi kuwalankhula kutali, navomereza kuti ali alendo ndi ogonera padziko. Ahebri 11:13
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi