Mtengo Wodziwitsa zabwino ndi zoipa komanso Mtengo wa Moyo, womwe Mulungu adauika m’munda wa Edeni, ndi fanizo komanso m’thunzi omwe Mulungu adalenga kuti aphunzitse anthu za Ufumu Wakumwamba.
Mulungu yekha ndi amene angatsegule njira ya ku Mtengo wa Moyo wa m’Munda wa Edeni womwe umatipatsa moyo wosatha.Kuti atipatse moyo wosatha, Yesu adatipatsa Paskha wa Pangano Latsopano zaka 2,000 zapitazo, ndipo Khristu Ahnsahnghong adatipatsa Paskha wa Chipangano Chatsopano mu m’badwo uno. Choncho, Khrisu Ahnsahnghong ndi Mulungu.
Khristu owona awonekeradi molingana ndi maumboni a m’Baibulo ndi aneneri. Monga oyera mtima a Mpingo woyamba adalalikirira kuti Yesu ndiye Khristu kulikonse komwe anapita, tiyenera kulalikira kuti Atate Ahnsahnghong omwe abweretsa Paskha wa Chipangano Chatsopano mu m’bado uno ndi Khristu yemwe wabweranso kachiwiri.
Iye wakudya thupi langa ndi kumwa mwazi wanga ali nao moyo wosatha ndipo Ine ndidzamuukitsa iye tsiku lomaliza. Pakuti thupi langa ndi chakudya ndithu ndi mwazi wanga ndi chakumwa ndithu… momwemo wondidya Ine iyeyu adzakhala ndi moyo chifukwa cha Ine.
Yohane 6:54–57
“Ndipo itadza nthawi yake, Iye anakhala pachakudya ndi ophunzira pamodzi ndi Iye.Ndipo anati kwa iwo,’ Ndinalakalaka ndithu kudya Paska uwu pamodzi ndinu ndisanayambe kusautsidwa’ ”
Luka 22:14–15
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi