Tingaone ubwino wa chikhulupiriro chathu mwa kumvera mawu a Mulungu.
Pamene tikhala m’choonadi kwa nthaŵi yaitali, kumvera ndi chikhulupiriro chathu ziyenera kukhala zozama.
Komabe, ngati tichita monga mwa kufuna kwathu monga Mfumu Sauli, Mulungu adzabweza chisomo chonse chimene Iye anatipatsa.
Khristu Ahnsahnghong, amene anabwera ngati Mpulumutsi mu m’badwo wa Mzimu Woyera, anaoneratu chilichonse kuyambira pa chiyambi mpaka mapeto a nthawi ya pansi pano ndipo anagwira ntchito ya chipulumutso kwa anthu onse.
Choncho, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhulupirira mawu Ake ndi kuwamvera muzochitika zonse monga Abrahamu ndi Gideoni.
Taonani, kumvera ndiko kokoma koposa nsembe, kutchera khutu koposa mafuta a nkhosa zamphongo.
Pakuti kupanduka kuli ngati choipa cha kuchita nyanga, ndi mtima waliuma uli ngati kupembedza milungu yachabe ndi maula. Popeza inu munakaniza mau a Yehova, Iyenso anakaniza inu, kuti simudzakhalanso mfumu.
1 Samueli 15:22-23
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi