Yesu ananena kuti anabwera padziko lapansi kudzafunafuna ndi kupulumutsa ochimwa.
Anthu, amene anachimwa kumwamba ndi kubwera padziko lapansi pano, ayenera kukwaniritsa kulapa kwathunthu pa Sabata ya Mapemphero kuchokera pa Phwando la Malipenga mpaka Tsiku la Chitetezero ndi kukumbatira chikondi cholengeza ku dziko lonse lapansi choonadi cha pangano latsopano limene Mulungu anakhazikitsa.
Pangano latsopano lili ndi nsembe ya Atate Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Chifukwa cha kupirira kwawo kopanda phokoso kwa ululu wa mtanda ndi nsembe ya imfa kuti apulumutse ana awo, njira yobwerera ku ufumu wakumwamba, ndiko kuti, chipata cha ufumu wakumwamba, chinali chotseguka kwa anthu lero.
Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iwo, Amene ali olimba safuna sing’anga; koma akudwala ndiwo.
Sindinadza Ine kuitana olungama, koma ochimwa kuti atembenuke mtima.
Luka 5: 31-32
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi