Makolo Akumwamba, Atate Ahnsahnghong
ndi Mulungu Amayi, akufuna kuti ana
Awo akhale ndi ziyeneretso zodzakhala
ansembe achifumu akumwamba.
N’chifukwa chake amafuna kuti ana
awo azindikire kufunika kwa ufumu
wakumwamba ngakhale kuti akukumana
ndi chisoni, zowawa komanso
mazunzo padziko lapansi.
Aliyense ali ndi zofooka
zake ngakhale kuti
sakudziwa bwino za izo.
Mulungu amayenga zofooka
zathu m'malo osiyanasiyana kuti
atipatse madalitso pamapeto pake.
Choncho, n’kofunika kumvera
mawu a Mulungu amene
amatitsogolera ku ufumu
wosatha wakumwamba.
Chifukwa chake tichite changu cha
kulowa mpumulowo, kuti wina angagwe
m'chitsanzo chomwe cha kusamvera.
Pakuti mau a Mulungu ali amoyo, ndi ochitachita,
ndi akuthwa koposa lupanga lakuthwa konsekonse,
napyoza kufikira kugawira moyo ndi mzimu,
ndi zimfundo ndi mafuta a m'mafupa,
nazindikiritsa zolingirira ndi zitsimikizo za mtima.
Ahebri 4:11-12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi