Adamu ndi Hava anamvera mawu a Satana, anadya chipatso choletsedwacho, ndipo anathamangitsidwa m’munda Mwa Edeni.
Mfumu Sauli anatsatira zimene anthu ankafuna, poona kuti mawu a Mulungu ndi aang’ono, ndipo anachotsedwa pampando wachifumu.
Momwemonso, mu nthawi ino, Mzimu Woyera ukhoza kuperekedwa kwa iwo okha amene amamvera mawu a Mulungu.
Pamene timvera mau a Mulungu, Mzimu Woyera amakhala nafe nthawi zonse, ndipo timakhala ndi moyo wodalitsika.
Popeza kuti anthu onse ndi opanda ungwiro, tiyenera kutsatira njira yangwiro ya Mulungu ndi kumvera mpaka mapeto kuti tikhale ndi moyo wopambana ndi kudzazidwa ndi Mzimu Woyera monga makolo athu achikhulupiriro.
Ndipo ife ndife mboni za zinthu izi; Mzimu Woyeranso, amene Mulungu anapatsa kwa iwo akumvera Iye.
Machitidwe 5:32
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi