Lerolino, ngati sitimvetsetsa mawu a m’Baibulo operekedwa ndi Mulungu, amene ali pakati pa chilengedwe chonse, sitidzazindikira Kudza Kwachiwiri kwa Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, Mkwatibwi, monga momwe anthu sanazindikire Yesu pa nthawi Yakubwera koyamba.
Kenako, tidzapereka kupembedza kopanda tanthauzo m’tchalitchi chimene Mulungu kulibe.
Monga momwe Davide analili ndi lamulo lofunikira pa ulamuliro wake pamene anali kulamulira Aisrayeli, palinso lamulo la pangano latsopano pakati pa Yesu amene analoseredwa monga Davide ndi anthu Ake.
Kudza kwachiwiri kwa Khristu Ahnsahnghong, amene anakwaniritsa maulosi onse a pampando wachifumu wa Davide, anatiphunzitsanso za pangano latsopano.
Atatero ana a Israele adzabwera, nadzafuna Yehova Mulungu wao, ndi Davide mfumu yao, nadzafika ndi mantha kwa Yehova, ndi ku ukoma wake masiku otsiriza.
Hoseya 3:5
Ndipo tsiku la mikate yopanda chotupitsa linafika . . .
Ndipo choteronso chikho, atatha mgonero, nanena, Chikho ichi ndi pangano latsopano m'mwazi wanga wothiridwa chifukwa cha inu.
Luka 22:7-20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi