Pa tsiku la chitetezero, pamene anthu alapa pamaso pa Mulungu machismo
onse amene anachita kumwamba ndi padziko lapansi lino, mwadala
ndi mosadziwa, iwo adzakhululukidwa machimo awo mwa chisomo
cha Mulungu ndi kupatsidwa mwayi wobwerera ku ufumu wakumwamba.
Monga Yesu anabwera ku dziko lapansi nati, “Lapani, pakuti Ufumu wa Kumwamba wayandikira,” Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi akuuzanso anthu kuti akwaniritse kulapa kwathunthu, kuthawa zionongeko, ndi kupulumutsidwa.
Ndipo Yesu anayankha, nati kwa iwo, Amene ali olimba safuna sing’anga; koma akudwala ndiwo.
Sindinadza Ine kuitana olungama, koma ochimwa kuti atembenuke mtima.
Luka 5: 31-32
Taonani, mkono wa Yehova sufupika, kuti sungathe kupulumutsa;
khutu lake silili logontha, kuti silingamve;
Yesaya 59:1–2
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi