Mpingo woyamba ndi atumwi sankasunga mapemphero
a Lamlungu kapena Khrisimasi.
Mulungu analemba m’Baibulo njira yoti anthu
alandire chikhululukiro cha machimo ndi kulowa
mu ufumu wakumwamba.
Iye anatsindika mobwerezabwereza kuti, “Musawonjezerepo kalikonse
kapena kuchotsapo kalikonse m’mawu a m’Baibulo.”
Masiku ano, mipingo padziko lapansi imakhulupirira
Mulungu Atate okha osati Mulungu Amayi,
koma ndi Mulungu Amayi amene amapereka
“moyo wosatha,” umene Mulungu analonjeza ana
ake.
Mulungu anachitira umboni za Mulungu Amayi
kudzera mwa zamoyo zonse zimene zinalengedwa
mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu kuphatikizapo
amuna ndi akazi, ndiponso kudzera mu
“mitochondria” yopezedwa ndi asayansi.
Ndichita umboni kwa munthu aliyense wakumva
mau a chinenero cha buku ili,
Munthu akaonjeza pa awa, adzamuonjezera Mulungu
miliri yolembedwa m’bukumu:
ndipo aliyense akachotsako pa mau a buku
la chinenero ichi, Mulungu adzam’chotsera gawo
lake pa mtengo wa moyo, ndi
m’mzinda woyerawo, ndi pa izi zilembedwa
m’bukumu.
Chivumbulutso 22:18-19
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi