Mulungu anabwera padziko lapansi kudzaonetsa anthu njira yopita kumwamba ndi njira yopita ku chikhululukiro cha machimo.
Komabe, anthu ambiri sanazindikire Yesu amene anabwera m’thupi koma anamulondalonda Iye, namutcha Iye wampatuko, pakunena, “Munthu wamba anganene bwanji kuti ndi Mulungu?” ndipo potsiriza anamupachika Iye.
Mofanana, masiku ano, sakhulupirira mwa Khristu Ahnsahnghong, amene anabweranso pa chipulumutso cha anthu.
Kuti tisakhale ngati anthu amene anapachika Yesu ndi kutembenuka kuchoka ku chipulumutso zaka 2,000 zapitazo, tiyenera kusunga maphwando a pangano latsopano mu Ziyoni, nyumba ya Mulungu amene analonjeza kubwera m’masiku otsiriza, ndi kulandira Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amene anabwera padziko lapansi pano m’thupi.
Ine ndi Atate ndife amodzi. Ayuda anatolanso
miyala kuti amponye Iye. . . .
Ayuda anamyankha Iye, Chifukwa cha
ntchito yabwino sitikuponyani miyala,
koma chifukwa cha mwano; ndi kuti Inu,
muli munthu, mudziyesera nokha Mulungu.
Yohane 10:30-33
kotero Khristunso ataperekedwa nsembe
kamodzi kukasenza machimo a ambiri,
adzaonekera pa nthawi yachiwiri
, wopanda uchimo, kwa iwo amene
amlindirira, kufikira chipulumutso.
Ahebri 9:28
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi