Chilichonse chomwe chinalembedwa m'Baibulo kwa zaka zoposa 1,600 chimagwirizana mongai ulosi ndi kukwaniritsidwa kwake. Ulosi wonena za Mfumu Kirusi ndi ulosi wonena za Yesu unalembedwanso m’Baibulo. Ngakhale kuti maulosi a m’Baibulo sanamvesetsedwe ndi anthu pamene analembedwa, onse anakwaniritsidwa.
Baibulo limatiuza tithawire ku Ziyoni kuti tipulumuke pamene tsoka lalikulu lomaliza ndi chionongeko chidzafika. Ziyoni—Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse Mpingo wa Mulungu, kumene kumasungidwa Maphwando a Mulungu, ndi malo othawirako ndi chipulumutso zimene Mulungu watilonjeza.
Nenani mu Yuda, lalikirani mu Yerusalemu, ndi kuti, Ombani lipenga m'dzikomo; fuulani, ndi kuti, Sonkhanani pamodzi, tilowe m'mizinda ya malinga. Kwezani mbendera kuyang'ana ku Ziyoni; thawani kuti mupulumuke, musakhale; pakuti ndidza ndi choipa chochokera kumpoto ndi kuononga kwakukulu. Yeremiya 4:5–6
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi