Abrahamu, Nowa, Mose, ndi Danieli anadalitsidwa chifukwa
chakuti anamvera mawu a Mulungu, mosasamala kanthu
za zovuta zimene anakumana nawo.
Mbiri yotereyi ya m’Baibulo imasonyeza kuti tiyenera
kukhala ndi chikhulupiriro cholimba chakuti Mulungu
alipo, mosasamala kanthu za mmene zinthu zilili.
Masiku khumi ayenera kuti anali okwanira kwa iwo kuti afike mu Kanani.
Komabe Aisraeli anakalowa patatha zaka 40 ndipo anaonongedwa mchipululu atatha kuwiringula ndi kunyinyilika pamene amangoyang'ana pa zomwe zimachitika patsogolo pawo
Chinali chifukwa chakuti analibe chikhulupiriro.
Momwemonso, lero, chinthu chofunika kwambiri m’chipululu cha
chikhulupiriro pamene tikulunjika ku Kanani wakumwamba
ndi kukhala ndi chikhulupiriro chonse m’mawu
a Mulungu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Koma chikhulupiriro ndicho chikhazikitso cha zinthu
zoyembekezeka, chiyesero cha zinthu zosapenyeka. Pakuti
momwemo akulu anachitidwa umboni. Ndi chikhulupiriro tizindikira
kuti maiko ndi a m'mwamba omwe anakonzedwa
ndi mau a Mulungu, kotero kuti zinthu
zopenyeka sizinapangidwe kuchokera mu zoonekazo.
Ahebri 11:1-3
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi