Mulungu anatsindika mobwerezabwereza
kwa Yoswa kukhala wolimba
mtima kwambiri atafika ku Kanani,
ndipo analamula Yona kulalikira mawu
a Mulungu molimba mtima mu likulu la dziko la adani.
Monga chonchi, ifenso
timafunika kulimba mtima
polalikila uthenga wabwino
wa pangano latsopano
padziko lonse lapansi.
Pokhulupirira kuti uthenga
wabwino wa Mulungu udzasintha
mdima kukhala kuwala kulikonse
kumene ulalikidwa, mamembala
a mpingo wa Mulungu, amene
adzalandira dziko la Kanani lauzimu,
amakwaniritsa ntchito ya Yoswa.
Monga momwe Yona
anachitira, iwo amalalikira
molimba mtima za chipulumutso
cha Khristu Ahnsahnghong
ndi Mulungu Amayi ku dziko lonse lapansi.
Khala wamphamvu, nulimbike
mtima, pakuti udzagawira anthu
awa dzikoli likhale cholowa chao,
ndilo limene ndinalumbirira makolo ao kuwapatsa.
Komatu khala wamphamvu, nulimbike
mtima kwambiri, kuti usamalire kuchita
monga mwa chilamulo chonse
anakulamuliracho Mose mtumiki wanga;
usachipatukire ku dzanja lamanja kapena
kulamanzere, kuti ukachite mwanzeru kulikonse umukako.
Yoswa 1:6-7
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi