“Kukhulupirira Mulungu” kumatanthauzakumvera ndi kugwiritsa ntchito mawu amene Iye amapereka.
Monga mkazi wa Loti anasandulika chulu cha mchere, ndipo Aisraeli anakhala akapoloa adani awo, momwemonso iwo amene samveramawu a Mulungu adzakumana ndi mavuto ofanana masiku ano.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhulupirira kuti ziphunzitso zoperekedwa ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi ndi njira yokhayo yopita ku chipulumutso chamuyaya kumwamba, ndikutsatira mosangalala malamulo Ake ndi mawu Ake onse, akuyembekezera mwachidwi, “Ndi mawu ati a madalitso omwe Mulungu adzatipatse ife lero?”
Atero Yehova, Mombolo wako, Woyera wa Israele, Ine ndine Yehova, Mulungu wako, amene ndikuphunzitsa kupindula, amene ndikutsogolera m’njira yoyenera iwe kupitamo.
Mwenzi utamvera malamulo anga mtendere wako ukanakhala ngati mtsinje, ndi chilungamo chako monga mafunde a nyanja;
Yesaya 48:17–18
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi