Mulungu, Mpulumutsi wa anthu, watipatsa madalitso a chikhululukiro cha machimo
ndi ufumu wamuyaya wakumwamba kupyolera mu Paska ndipo analengeza mwamphamvu
kuti iwo amene amasunga Paska adzazindikiridwa monga anthu a Mulungu
amene adzalandira unzika wakumwamba ndi kukapeza. chipulumutso.
Yesu yemwe anabwera zaka 2,000 zapitazo komanso Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi mu m'badwo uno nthawi zonse amatiphunzitsa kuti kutanira pa Mulungu ndi milomo yathu popanda kusunga Paskha ndi chikhulupiriro chosadziwika bwino.
Komanso chifukwa chimene Mulungu anaperekera Paska Yachiwiri kwa anthu
amene sanathe kusunga pa nthawi yake ndi chakuti
Paska ndi phwando lofunika kwambiri limene limasiyanitsa anthu oona.
Ana a Israele achite Paska pa nyengo yoikidwa. . . .
Pamenepo panali amuna, anadetsedwa ndi mtembo wa munthu,
ndipo sanakhoze kuchita Paska tsiku lomwelo; . . .
Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,
. . . chifukwa cha mtembo, kapena pokhala paulendo, koma azichitira Yehova Paska.
Mwezi wachiwiri, tsiku lake lakhumi ndi chinai, madzulo, auchite; . . .
Munthu akakhala woyera, . . .
koma akaleka kuchita Paska, amsadze munthuyo kwa anthu a mtundu wake; . . .
Numeri 9:2-13
Inde chomwecho pa zipatso zao mudzawazindikira iwo.
Si yense wakunena kwa Ine, Ambuye, Ambuye, adzalowa mu Ufumu wa Kumwamba; koma wakuchitayo chifuniro cha Atate wanga wa Kumwamba.
Mateyu 7:20-21
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi