Monga momwe Mulungu anali ndi cholinga chachikulu chodalitsa Aisraele pambuyo pa zaka 40 m’chipululu, lerolino, Mulungu atha kuika mavuto ndi zopinga panjira yathu ya chikhulupiriro, koma cholinga chake chachikulu ndikungwira miyoyo yathu ndi kutipatsa madalitso a ufumu wa kumwamba.
Dziko lapansi ndi ndende yauzimu kumene angelo a kumwamba amene anachita machimo akupha anaponyedwa kudzakhala. N’chifukwa chake pa dziko lino lapansi, nthawi za zowawa ndi za mavuto zimachitika pafupipafupi kuposa za mtendere ndi chimwemwe. Kuti afafanize machimo a anthuwa, Mulungu anakhetsa Mwazi Wake pamtanda ndipo anatitsegulira njira yobwerera ku ufumu wa kumwamba kudzera mu Paska wa pangano latsopano, njira yopita ku chikhulukukiro cha machimo.
amene anakudyetsani m'chipululu ndi mana, amene makolo anu sanawadziwe; kuti akuchepetseni, ndi kuti akuyeseni, kuti akuchitireni chokoma potsiriza panu; Deuteronomo 8:16
Pakuti Mwana wa Munthu anadza kufunafuna ndi kupulumutsa chotayikacho. Luka 19:10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi