Kuti titsatire bwino njira ya Khristu, tiyenera kusenza mtanda wathu.
Yesu, yemwe ndi Mulungu, ananyamula cholemetsa cha mtanda kuti apulumutse anthu, ndipo makolo achikhulupiriro monga Mose ndi mtumwi Paulo anasenza mtanda wawo wa masautso ndi chimwemwe. Momwemonso, ifenso tiyenera kunyamula mtanda wathu ndi kuyenda m’njira ya kuvutika chifukwa cha chipulumutso.
Monga momwe mtumwi Paulo anaonera kuvutika konse monga madalitso, kutsatira njira ya mtanda wa Khristu, mamembala a Mpingo wa Mulungu mosangalala amasenza mtanda wawo nthawi iliyonse ndikutsatira njira ya Mulungu ndi chikhulupiriro cholimba, osaiwala kuyamika Mulungu.
Odala ali akuzunzidwa chifukwa cha chilungamo: chifukwa uli wao Ufumu wa Kumwamba. Odala muli inu m’mene adzanyazitsa inu, nadzazunza inu, nadzakunenerani monama zoipa zilizonse chifukwa cha Ine. Sekerani, sangalalani: chifukwa mphotho yanu ndi yaikulu mu Mwamba: pakuti potero anazunza aneneri anakhalawo musanabadwe inu. Mateyu 5:10–12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi