Kudzera mu dongosolo la m’banja la padziko lapansi, Mulungu watiuza kuti pali banja lakumwamba.
Monga ana apadziko lapansi amalandira thupi ndi mwazi wa makolo awo, ana akumwamba ayenera kulandira thupi ndi mwazi wa Mulungu Atate ndi Mulungu Amai kudzera mu mkate ndi vinyo wa Paska.
Anthu oterowo okha angathe kutchula Mulungu “Atate” ndi “Amai” monga ana akumwamba.
Masiku, mamembala a Mpingo wa Mulungu amatamandidwa chifukwa cha ntchito zawo zabwino padziko lonse lapansi chifukwa amakonda anthu onse ndi chikondi ndi nsembe zomwe aphunzira kuchokera kwa Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai, komanso chifukwa ulemerero wa Yerusalemu wadzaza dziko lonse lapansi monga momwe Baibulo linanenera.
Ndaika alonda pa malinga ako, Yerusalemu; iwo sadzakhala chete usana pena usiku; inu akukumbutsa Yehova musakhale chete, ndipo musamlole akhale chete, kufikira Iye atakhazikitsa naika Yerusalemu akhale tamando m’dziko lapansi. Yesaya 62:6–7
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi