Mawu onse a Mulungu olembedwa m'Baibulo amakwaniritsidwa mosalephera. Baibulo linachitira umboni za Yesu amene anabwera zaka 2,000 zapitazo, ndipo limachitira umboni za Ntchito ya Chipulumutso imene idzachitike mu m'badwo wa Mzimu Woyera ndi Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai, amene abwera monga Mzimu ndi Mkwatibwi.
Baibulo limaneneratu kuti anthu amene adzapulumutsidwe—amene ali ndi chikhulupiriro chopambana m’dziko lino lolamulidwa ndi Satana—ndi otsala a mbewu ya Mkazi, amene amasunga malamulo a Mulungu. Limachitiranso umboni kuti iwo, monga Isake, adzalandira cholowa cha ufumu wa kumwamba kudzera mwa Amai Akumwamba.
Musanthula m'malembo, popeza muyesa kuti momwemo muli nao moyo wosatha; ndipo akundichitira Ine umboni ndi iwo omwewo... Yohane 5:39
Ndipo chinaponyedwa pansi chinjoka chachikulu, njoka yokalambayo, iye wotchedwa mdierekezi ndi Satana, wonyenga wa dziko lonse; chinaponyedwa pansi kudziko, ndi angelo ake anaponyedwa naye pamodzi. Ndipo chinjoka chinakwiya ndi mkazi, nichinachoka kunka kuchita nkhondo ndi otsala a mbeu yake, amene asunga malamulo a Mulungu, nakhala nao umboni wa Yesu. Chivumbulutso 12:9, 17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi