Mawu akuti, “Musanyadire za mawa,” ndi chikumbutso cha Mulungu kuti n’kofunika kuti tisachedwetse mwayi wathu wa dalitso mpaka mawa losatsimikizika. M’malo mwake, tiyenera kugawana chikondi chathu ndi abale ndi alongo athu lero, kupemphera lero, kulapa zolakwa zathu lero, ndikulalikira uthenga wa chipulumutso lero.
Kudzera m'mbiri ya mdindo wa Kandake, mfumukazi ya Aitiopiya, amene anabatizidwa atangomvetsetsa chowonadi ali panjira, ndi mdindo wa ndende ndi banja lake, omwe anabatizidwa pakati pa usiku osadikira mbandakucha, Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai atiphunzitsa kuti tingathe kupulumutsa dziko lapansi pokhapokha pamene tilalikira uthenga wabwino wa pangano latsopano—womwe ndi uthenga wa chipulumutso—pompopompo pamene tawuzindikira.
Usanyadire zamawa, popeza sudziwa tsiku lina lidzabala chiyani? Miyambo 27:1
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi