Yesu Mwiniwake anapereka chitsanzo chopulumutsa anthu ku uchimo kudzera mu ulaliki. Anatipatsa ntchito yokhala antchito a pangano latsopano, ponena kuti, “Pulumutsani dziko lapansi.” Choncho, sitiyenera kukhala ngati Esau, amene ankangochita zimene ankafuna, koma tikhale ngati Yakobo, amene anayambira kuchita zimene anayenera kuchita. Pokhapo ndi pamene tingalandire madalitso amene Mulungu amapereka.
Zotsatira za iwo amene amachita zomwe ayenera kuchita poyerekeza ndi omwe sachita, ndiko kusiyana pakati pa ufumu wa kumwamba ndi gehena. Monga momwe ntchito yodabwitsa ya Mzimu Woyera inalili nthawi zonse ndi atumwi amene anakhala ndi moyo wolalikira monga Yesu, ntchito yathu tsopano ndiyo kulengeza chipulumutso cha Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai.
amenenso anatikwaniritsa ife tikhale atumiki a pangano latsopano—si la chilembo, koma la mzimu; pakuti chilembo chipha, koma mzimu uchititsa moyo. 2 Akorinto 3:6
Ndipo ananena nao, Tiyeni kwina—kumidzi ili pafupi apa, —kuti ndilalikire komwekonso; pakuti ndadzera ntchito imene.” Marko 1:38
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi