Baibulo si nthano chabe; ndi mawu a moyo ochokera kwa Mulungu, amene amatsimikizira tsogolo la anthu. Kudzera mu maulosi operekedwa kwa Daniele okhudza kukwera ndi kugwa kwa maufumu pambuyo pa Ufumu wa Babulo, kufotokozera za mayendedwe a madzi ndi mfundo zasayansi monga dziko lapansi kupachikidwa mu mlengalenga zomwe zinavumbulutsidwa kwa Yobu zaka 3,500 zapitazo, tingathe kudziwa motsimikiza kuti Baibulo ndi mawu a Mulungu.
Mtumwi Yohane anaona oyera mtima omwe adzapulumutsidwe—iwo amene mayina awo analembedwa m’buku la moyo la Mwanawankhosa. Masiku ano, mamembala a Mpingo wa Mulungu, amene mayina awo alembedwa m’buku la moyo monga momwe Mtumwi Yohane adaneneratu, akukwaniritsa maulosi, pokhudzidwa kwambiri ndi ulemerero wosatha umene adzasangalale nawo mu ufumu wa kumwamba.
Koma opatulika a Wam'mwambamwamba adzalandira ufumuwo, ndi kukhala nao ufumu kosatha, kunthawi zonka muyaya. Daniele 7:18
Ndipo sikudzakhalanso usiku; ndipo sasowa kuunika kwa nyali, ndi kuunika kwa dzuwa; chifukwa Ambuye Mulungu adzawaunikira; ndipo adzachita ufumu kunthawi za nthawi. Chivumbulutso 22:5
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi