Anthu anapusitsidwa ndi Satana mu ufumu wa kumwamba ndipo, atapandukira Mulungu, anaponyedwa padziko lapansi chifukwa cha uchimo umenewo. Kuti afune ana otayika kuchokera kumwamba, kuwapatsa chikhulukukiro cha machimmo, ndi kuwabweretsanso mu ufumu wa kumwamba, Yesu anabwera zaka 2,000 zapitazo, ndipo Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai abwera mu m'badwo uno.
Kudzera mu mafanizo a matalente ndi a mina, Yesu anaphunzitsa mwatsatanetsatane mmene ana amene adziwa chikondi cha Mulungu angamukondweretsere Mulungu. Monga momwe Mulungu walalikirira mosalekeza kuti afunefune ana otayika a kumwamba, ifenso tiyenera kufunafuna abale ndi alongo athu otayika ndiyo mphatso yamtengo wapatali kwambiri imene tingapereke kwa Mulungu.
Ndipo m'mawa mwake anauka usikusiku, natuluka namuka kuchipululu, napemphera kumeneko. Ndipo ananena nao, Tiyeni kwina, kumidzi ili pafupi apa, kuti ndilalikire komwekonso; pakuti ndadzera ntchito imene. Marko 1:35, 38
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi