Amene amaima ku mbali ya Mulungu amakumbukira lamulo Lake, Tsiku la Sabata, ndi kulisunga mopatulika. Mosiyana mbali inayi, amene ali ku mbali ya Satana amatsutsa Tsiku la Sabata, limene liri chifuniro cha Mulungu. Baibulo limalemba kuti iwo pamapeto pake adzanyenga dziko lonse ndi kulitsogolera ku chiwonongeko.
Anthu a Mulungu amene amaima ku mbali ya Mulungu nthawi zonse amasunga malamulo Ake. Mtumwi Yohane anafotokoza amene amatsatira Mwanawankhosa kulikonse kumene apita monga “oyera mtima.” Iye anati iwo ndi amene amasonyeza kupirira kwawo mwa kusunga malamulo a Mulungu mpaka ku mapeto enieni.
Pano pali chipiriro cha oyera mtima, cha iwo akusunga malamulo a Mulungu, ndi chikhulupiriro cha Yesu. Chivumbulutso 14:12
Udzikumbukira tsiku la Sabata, kuti likhale lopatulika. Eksodo 20:8
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi