Mpingo umene Yesu anapereka chipulumutso pamene anabwera padziko lapansi zaka 2,000 zapitazo ndipo anakhazikitsa Paska wa pangano latsopano, ndi Mpingo umene kumapezeka oyera mtima a Mpingo woyamba monga mtumwi Paulo, Petro, ndi Yohane anali Mpingo wa Mulungu. Komabe, cha mzaka za m'ma 400, malamulo a Mulungu anachotsedwa, ndipo miyambo yachikunja inalowa mu tchalitchi. Kuwala kwa chipulumutso kunasowa ndipo Mbado Wamdima unayamba.
Malinga ndi ulosi wa m'Baibulo, Khristu Ahnsahnghong anakhazikitsa Mpingo wa Mulungu ku Korea mu 1964 ndipo anatsogolera Mpingo ndi choonadi cha Paska wa pangano latsopano zochokera m'Baibulo ndi maziko a aneneri. Iwo anadziwitsa ana Awo za Mulungu Amayi, amene anabwera padziko lapansi kudzapulumutsa anthu, ponena kuti, "Petro anatsatira Yesu, ndipo ine ndikutsatira Amayi."
[K]wa Mpingo wa Mulungu wakukhala mu Korinto, ndiwo oyeretsedwa mwa Khristu Yesu, oitanidwa akhale oyera mtima, . . . 1 Akorinto 1:2
[O]mangika pa maziko a atumwi ndi aneneri, pali Khristu Yesu mwini, mwala wa pangodya; Aefeso 2:20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi