Popeza Yesu anabwera ngati munthu, anadya chakudya cha anthu, ndipo anakhala monga mmene anthu amakhalira, anthu osaŵerengeka analephera kumuzindikira kuti ndi Mulungu ndipo anamukana. Ndi chifukwa chake Baibulo limatiphunzitsa kuti mzimu uliwonse umene umavomereza kuti Yesu anabwera m'thupi umachokera kwa Mulungu, ndipo mzimu uliwonse umene sumavomereza izi ndi mzimu wa wotsutsakhristu.
Mu m'badwo wa Mzimu Woyera, Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai anabwera kudzapulumutsa mtundu wa anthu. Kuti mtundu wa anthu ulandire dalitso la chipulumutso kuchokera kwa Mulungu, choyamba uyenera kusiya kalingaliridwe kake ndi kukhulupirira ulosi wa m’Baibulo, umene umanena kuti Mulungu adzabweranso kachiwiri m’thupi.
amene afuna anthu onse apulumuke, nafike pozindikira choonadi. Pakuti pali Mulungu mmodzi, ndi Mtetezi mmodzi pakati pa Mulungu ndi anthu, ndiye munthu, Khristu Yesu, ... 1 Timoteo 2:4–5
M'menemo muzindikira Mzimu wa Mulungu: mzimu uliwonse umene uvomereza kuti Yesu Khristu anadza m'thupi, uchokera mwa Mulungu; ...ndipo mzimu uliwonse umene suvomereza Yesu suchokera kwa Mulungu; ndipo uwu ndiwo mzimu wa wokana Khristu, ... 1 Yohane 4:2–3
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi