Mulungu analenga amene ali ndi unzika wakumwamba ndi mitima yomwe imayamikira Sabata, Paska ndi maphwando asanu ndi awiri mu nthawi zitatu kuti asunge malamulo Ake. Choncho, kwa onse amene amatchula Mulungu ndi milomo yawo koma amatsatira lamulo la mulungu wa dzuwa m’malo mwa lamulo la Mulungu, Iye amawachenjeza za tchimo lawo, ponena kuti: “Sindikudziwani.”
Ngakhale dziko lonse litasinthika, chinthu chimodzi chomwe sichisintha ndi lamulo la Mulungu. Yesu anasunga Paska zaka 2,000 zapitazo, ndipo Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai nawonso anausunga m'badwo wa Mzimu Woyera. Kutsatira chitsanzo Chawo posunga Paska ndicho chikhulupiriro cholondola, chokhazikika pa Mulungu.
Si yense wakunena kwa Ine, Ambuye, Ambuye, adzalowa mu Ufumu wa Kumwamba; koma wakuchitayo chifuniro cha Atate wanga wa Kumwamba. Ndipo pamenepo ndidzafukulira iwo, Sindinakudziwani inu nthawi zonse; chokani kwa Ine, inu akuchita kusaweruzika. Mateyu 7:21–23
Munthu akakhala woyera, wosakhala paulendo, koma akaleka kuchita Paska, amsadze munthuyo kwa anthu a mtundu wake... munthuyu asenze kuchimwa kwake. Numeri 9:13
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi