Popeza mabuku 66 a m’Baibulo ali ndi njira yofikira kwa Mpulumutsi ndi nzeru yodziwira choonadi kuchokera ku bodza, Mulungu akutichenjeza kuti tisawonjezere kapena kuchotsa kalikonse m’Baibulo, koma kuti titsatira malingana ndi mawu a Mulungu okha.
Zaka zikwi ziwiri zapitazo, Yesu yekha anafuula, “Idzani kwa Ine kuti mulandire madzi a moyo,” koma Iye watiphunzitsa kuti tsopano tiyenera kubwera kwa Mzimu ndi Mkwatibwi kuti tilandire madzi a moyo ndi kukhala ndi moyo wosatha.
Yesaya analosera kuti Mulungu adzatsogolera ana ake ku kasupe wa madzi amoyo, ndipo Mulungu Ahnsahnghong, Mzimu Woyera, amene anakwaniritsa maulosi onse a m’Baibulo, watsogolera anthu kwa Amai Yerusalemu Akumwamba, Mkwatibwi wa Mzimu Woyera komanso gwero la madzi a moyo.
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena, Idzani. Ndipo wakumva anene, Idzani. Ndipo wakumva ludzu adze; iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere. Chivumbulutso 22:17
Atero Yehova, Nthawi yondikomera ndakuyankha Iwe, ndi tsiku la chipulumutso ndakuthandiza; . . . pakuti Iye amene wawachitira chifundo, adzawatsogolera, ngakhale pa akasupe a madzi adzawatsogolera. Yesaya 49:8–10
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi